Psalms 134:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akudalitseni Chauta amene amakhala ku Ziyoni, amene adalenga kumwamba ndi dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova, ali m'Ziyoni, akudalitseni; ndiye amene analenga kumwamba ndi dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova wolenga kumwamba ndi dziko lapansi, akudalitseni kuchokera mʼZiyoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova, ali m'Ziyoni, akudalitseni; Ndiye amene analenga kumwamba ndi dziko lapansi.