Psalms 135:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye amene adaononga mitundu yambiri ya anthu, ndi kupha mafumu amphamvu aja,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiye amene anapanda amitundu ambiri, napha mafumu amphamvu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anakantha mitundu yambiri ya anthu ndi kupha mafumu amphamvu:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiye amene anapanda amitundu ambiri. Napha mafumu amphamvu;