Psalms 135:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sihoni, mfumu ya Aamori, ndi Ogi, mfumu ya ku Basani, pamodzi ndi maufumu onse a ku Kanani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sihoni mfumu ya Aamori, ndi Ogi mfumu ya Basani, ndi maufumu onse a Kanani:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sihoni mfumu ya Aamori, Ogi mfumu ya Basani, ndi maufumu onse a ku Kanaani;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sihoni mfumu ya Aamori, Ndi Ogi mfumu ya Basana, Ndi maufumu onse a Kanani: