Psalms 135:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapereka dziko lao kuti likhale choloŵa, choloŵa cha Aisraele, anthu ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapereka dziko lao likhale chosiyira, chosiyira cha kwa Israele anthu ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo anapereka dziko lawo ngati cholowa, cholowa cha anthu ake Aisraeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapereka dziko lao likhale cosiyira, Cosiyira ca kwa Israyeli anthu ace.