Psalms 135:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dzina lanu, Inu Chauta, nlamuyaya, kutchuka kwanu ndi kwa pa mibadwo yonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dzina lanu, Yehova, likhala kosatha; chikumbukiro chanu, Yehova, kufikira mibadwomibadwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzina lanu, Inu Yehova, ndi losatha mpaka muyaya, mbiri yanu, Inu Yehova, idziwika mibado yonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dzina lanu, Yehova, likhala kosatha; Cikumbukilo canu, Yehova, kufikira mibadwo mibadwo.