Psalms 135:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti Chauta adzaweruza anthu ake kuti alibe mlandu, adzachitira chifundo atumiki ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova adzaweruza anthu ake, koma adzaleka atumiki ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Yehova adzaonetsa kuti anthu ake ngosalakwa, ndipo adzachitira chifundo atumiki ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova adzaweruza anthu ace, Koma adzaleka atumiki ace.