Psalms 135:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mafano a mitundu ina ya anthu ndi asiliva ndi agolide chabe, ndi opangidwa ndi manja a anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mafano a amitundu ndiwo siliva ndi golide, ntchito ya manja a anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mafano a mitundu ya anthu ndi siliva ndi golide, opangidwa ndi manja a anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mafano a amitundu ndiwo siliva ndi golidi, Nchito ya manja a anthu.