Psalms 135:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakamwa ali napo, koma salankhula, maso ali nawo, koma sapenya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakamwa ali napo koma osalankhula; maso ali nao, koma osapenya;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakamwa ali napo koma sayankhula maso ali nawo, koma sapenya;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakamwa ali napo koma osalankhula; Maso ali nao, koma osapenya;