Psalms 135:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Makutu ali nawo, koma saamva, ndipo alibe mpweya m'kamwa mwao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
makutu ali nao, koma osamva; inde, pakamwa pao palibe mpweya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
makutu ali nawo, koma sakumva ndipo mʼkamwa mwawo mulibe mpweya uliwonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Makutu ali nao, koma osamva; Inde, pakamwa pao palibe mpweya.