Psalms 135:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
inu amene mumatumikira m'Nyumba ya Chauta, m'mabwalo a Nyumba ya Mulungu wathu!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inu akuimirira m'nyumba ya Yehova, m'mabwalo a nyumba ya Mulungu wathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amene mumatumikira mʼnyumba ya Yehova, mʼmabwalo a nyumba ya Mulungu wathu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inu akuimirira m'nyumba ya Yehova, M'mabwalo a nyumba ya Mulungu wathu.