Psalms 135:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti ndimadziŵa kuti Chauta ndi wamkulu, kuti Chauta, Mulungu wathu, ndi wamphamvu kupambana milungu yonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndidziwa kuti Yehova ndi wamkulu, ndi Ambuye wathu aposa milungu yonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikudziwa kuti Yehova ndi wamkulu, kuti Ambuye athu ndi wamkulu kuposa milungu yonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndidziwa kuti Yehova ndi wamkuru, Ndi Ambuye wathu aposa milungu yonse.