Psalms 135:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye amene adapha ana achisamba a ku Ejipito, ana a anthu ndi a nyama omwe,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anapanda oyamba a Ejipito, kuyambira munthu kufikira zoweta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anakantha ana oyamba kubadwa a Igupto, ana oyamba kubadwa a anthu ndi nyama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anapanda oyamba a Aigupto, Kuyambira munthu kufikira zoweta.