Psalms 136:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapha ana achisamba a ku Ejipito, pakuti chikondi chake nchamuyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye amene anapandira Aejipito ana ao oyamba; pakuti chifundo chake nchosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amene anakantha ana woyamba kubadwa a Igupto, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye amene anapandira Aaigupto ana ao oyamba: Pakuti cifundo cace ncosatha.