Psalms 136:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi dzanja lamphamvu ndi mkono wotambalitsa, pakuti chikondi chake nchamuyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi dzanja lamphamvu, ndi mkono wotambasuka; pakuti chifundo chake nchosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi dzanja lamphamvu ndi mkono wotambasuka, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi dzanja lamphamvu, ndi mkono wotambasuka: Pakuti cifundo cace ncosatha.