Psalms 136:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapha Sihoni, mfumu ya Aamori, pakuti chikondi chake nchamuyaya,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sihoni mfumu ya Aamori; pakuti chifundo chake nchosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Siloni mfumu ya Aamori, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sihoni mfumu ya Aamori; Pakuti cifundo cace ncosatha.