Psalms 136:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapha Ogi, mfumu ya ku Basani, pakuti chikondi chake nchamuyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Ogi mfumu ya Basani; pakuti chifundo chake nchosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ogi mfumu ya Basani, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ogi mfumu ya Basana: Pakuti cifundo cace ncosatha.