Psalms 136:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Napereka dziko la mafumuwo kuti likhale choloŵa, pakuti chikondi chake nchamuyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapereka dziko lao likhale chosiyira; pakuti chifundo chake nchosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Napereka dziko lawo ngati cholowa, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaperekadzikolaolikhale cosiyira; Pakuti cifundo cace ncosatha.