Psalms 136:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adalenga zakumwamba ndi nzeru zake, pakuti chikondi chake nchamuyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amene analenga zakumwamba mwanzeru; pakuti chifundo chake nchosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amene mwachidziwitso chake anapanga mayiko akumwamba, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amene analenga zakumwamba mwanzeru: Pakuti cifundo cace ncosatha.