Psalms 136:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adayala dziko lapansi pa madzi, pakuti chikondi chake nchamuyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amene anayala dziko lapansi pamwamba pa madzi; pakuti chifundo chake nchosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amene anayala dziko lapansi pamwamba pa madzi, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amene anayala dziko lapansi pamwamba pa madzi: Pakuti cifundo cace ncosatha.