Psalms 137:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'mbali mwa mitsinje ya ku Babiloni, kumeneko tidakhala pansi nkumalira tikukumbukira Ziyoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ku mitsinje ya ku Babiloni, kumeneko tinakhala pansi, inde tinalira, pokumbukira Ziyoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmbali mwa mitsinje ya ku Babuloni tinakhala pansi ndi kulira pamene tinakumbukira Ziyoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ku mitsinje ya ku Babulo, Kumeneko tinakhala pansi, inde tinalira, Pokumbukila Ziyoni.