Psalms 137:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumeneko anthu otigwira ukapolo adatipempha kuti tiimbe nyimbo. Otizunza adatipempha kuti tisangalale, adati, “Tatiimbiraniko nyimbo ya ku Ziyoni.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza pamenepo akutigwirawo anatifunsa nyimbo ndipo akutizunza anafuna tisekere, ndi kuti, Mutiimbire nyimbo imodzi ya ku Ziyoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti anthu otigwira ukapolo anatipempha kuti tiyimbe nyimbo. Otizunza athu anafuna nyimbo zachisangalalo; iwo anati, “Tiyimbireni imodzi mwa nyimbo za ku Ziyoni!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza pamenepo akutigwirawo anatifunsa nyimbo, Ndipo akutizunza anafuna tisekere, Ndi kuti, Mutiyimbire nyimbo imodzi ya ku Ziyoni.