Psalms 137:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikakuiŵala iwe Yerusalemu, dzanja langa lamanja liwume.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikakuiwalani, Yerusalemu, dzanja lamanja langa liiwale luso lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikakuyiwala iwe Yerusalemu, dzanja langa lamanja liyiwale luso lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikakuiwalani, Yerusalemu, Dzanja lamanja langa liiwale luso lace.