Psalms 137:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mzinda wa Babiloni, iwe woyenera kuwonongedwawe, adzakhala wodala munthu amene adzakubwezera zimene watichita ifezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwana wamkazi wa ku Babiloni, iwe amene udzapasulidwa; wodala iye amene adzakubwezera chilango monga umo unatichitira ife.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe mwana wa mkazi wa Babuloni, woyenera kuwonongedwa, wodalitsika ndi yemwe adzakubwezera pa zimene watichitira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwana wamkazi wa ku Babulo, iwe amene udzapasulidwa; Wodala iye amene adzakubwezera cilango Monga umo unaticitira ife.