Psalms 137:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzakhala wodala munthu amene adzatenga makanda ako ndi kuŵakankhanthitsa ku thanthwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wodala iye amene adzagwira makanda ako, ndi kuwaphwanya pathanthwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amene adzagwira makanda ako ndi kuwakankhanthitsa pa miyala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wodala iye amene adzagwira makanda ako, Ndi kuwaphwanya pathanthwe.