Psalms 138:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikukuthokozani Inu Chauta ndi mtima wanga wonse. Ndikuimba nyimbo zokutamandani pamaso pa milungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Salimo la Davide. Ndidzakuyamikani ndi mtima wanga wonse; ndidzaimba zakukulemekezani patsogolo pa milungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salimo la Davide. Ndidzakuyamikani Yehova ndi mtima wanga wonse; ndidzayimba nyimbo zokutamandani pamaso pa “milungu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzakuyamikani ndi mtima wangawonse; Ndidzayimba zakukulemekezani patsogolo pa milungu,