Psalms 138:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mafumu onse a m'dziko adzakutamandani, Inu Chauta, chifukwa amva mau a pakamwa panu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mafumu onse a pa dziko lapansi adzakuyamikani, Yehova, popeza adamva mau a pakamwa panu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mafumu onse a dziko lapansi akuyamikeni Yehova, pamene amva mawu a pakamwa panu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mafumu onse a pa dziko lapansi adzakuyamikani, Yehova, popeza adamva mau a pakamwa panu.