Psalms 138:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale Chauta ndi wamphamvu, amasamalira anthu otsika, koma anthu odzikuza amaŵadziŵira chapatali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Angakhale Yehova ngwokwezeka, apenyanso wopepukayo; koma wodzikuza amdziwira kutali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale kuti Yehova ngokwezeka, amasamalira odzichepetsa, koma anthu onyada amawadziwira chapatali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Angakhale Yehova ngwokwezeka, apenyanso wopepukayo; Koma wodzikuza amdziwira kutali.