Psalms 138:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adzaona kuti cholinga chake pa ine chichitikedi. Chikondi chanu, Inu Chauta, nchamuyaya. Muipitirize ntchito imene mwaiyambayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova adzanditsirizira za kwa ine: Chifundo chanu, Yehova, chifikira kunthawi zonse: Musasiye ntchito za manja anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova adzakwaniritsa cholinga chake pa ine; chikondi chanu chosasinthika Yehova, ndi chosatha musasiye ntchito ya manja anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova adzanditsirizira za kwa ine: Cifundo canu, Yehova, cifikira ku nthawi zonse: Musasiye nchito za manja anu.