Psalms 139:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta mwafufuzafufuza, ndipo mwandidziŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo; Salimo la Davide. Munandisanthula, Yehova, nimundidziwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Salimo la Davide. Inu Yehova, mwandisanthula ndipo mukundidziwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munandisanthula, Yehova, nimundidziwa.