Psalms 139:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikanena kuti, “Mdima undiphimbe, kuŵala kumene kwandizinga kusanduke mdima,”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndikati, Koma mdima undiphimbe, ndi kuunika kondizinga kukhale usiku.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikanena kuti, “Zoonadi, mdima udzandibisa ndithu ndipo kuwunika kukhale mdima mondizungulira,”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndikati, Koma mdima undiphimbe, Ndi kuunika kondizinga kukhale usiku: