Psalms 139:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ngakhale mdimawo, kwa Inu si mdima konse, kwa Inu usiku umaŵala ngati usana, mdima uli ngati kuŵala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ungakhale mdima sudetsa pamaso panu, koma usiku uwala ngati usana; mdima ukunga kuunika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
komabe mdimawo sudzakhala mdima kwa Inu; usiku udzawala ngati masana, pakuti mdima uli ngati kuwunika kwa Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ungakhale mdima sudetsa pamaso panu, Koma usiku uwala ngati usana: Mdima ukunga kuunika.