Psalms 139:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja ndinu mudapanga za m'kati mwanga, mudandiwumba m'mimba mwa amai anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Inu munalenga impso zanga; munandiumba ndisanabadwe ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Inu munalenga za mʼkati mwanga; munandiwumba pamodzi mʼmimba mwa amayi anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Inu munalenga imso zanga; Munandiumba ndisanabadwe ine.