Psalms 139:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mapangidwe anga sadabisike pamaso panu pamene ndinkapangidwa mwachinsinsi, pamene ndinkaumbidwa mwaluso m'mimba mwa amai anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Thupi langa silinabisikira Inu popangidwa ine mobisika, poombedwa ine monga m'munsi mwake mwa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mapangidwe anga sanabisike pamaso panu pamene ndimapangidwa mʼmalo achinsinsi, pamene ndinkawumbidwa mwaluso mʼmimba ya amayi anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Thupi langa silinabisikira Inu popangidwa ine mobisika, Poombedwa ine monga m'munsi mwace mwa dziko lapansi.