Psalms 139:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maso anu adandiwona ndisanabadwe. Masiku a moyo wanga mudaŵalemberatu m'buku mwanu, asanayambe nkuŵerengedwa komwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndisanaumbidwe ine maso anu anandipenya, ziwalo zanga zonse zinalembedwa m'buku mwanu, masiku akuti ziumbidwe, pakalibe chimodzi cha izo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Maso anu anaona thupi langa lisanawumbidwe. Masiku onse amene anapatsidwa kwa ine, analembedwa mʼbuku lanu asanayambe nʼkuwerengedwa komwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndisanaumbidwe ine maso anu anandipenya, Ziwalo zanga zonse zinalembedwa m'buku mwanu, Masiku akuti ziumbidwe, Pakalibe cimodzi ca izo.