Psalms 139:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikadakonda kuti muwononge anthu oipa, Inu Mulungu, ndipo kuti anthu okhetsa magazi andichokere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Indedi, mudzaomba woipa, Mulungu: Ndipo amuna inu okhumba mwazi, chokani kwa ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi bwino mukanangopha anthu oyipa, Inu Mulungu! Chokereni inu anthu owononga anzanu!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Indedi, mudzaomba woipa, Mulungu: Ndipo amuna inu nkhumba mwazi, cokani kwa ine.