Psalms 139:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mumadziŵa pamene ndikhala pansi, pamenenso ndidzuka, mumazindikira maganizo anga muli kutali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inu mudziwa kukhala kwanga ndi kuuka kwanga, muzindikira lingaliro langa muli kutali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mumadziwa pamene ndikhala pansi ndi pamene ndidzuka; mumazindikira maganizo anga muli kutali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inumudziwakukhalakwangandi kuuka kwanga, Muzindikira lingaliro langa muli kutali.