Psalms 139:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthuwo amakunenani zinthu zoipa, namakuukirani ndi mtima woipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza anena za Inu moipa, ndi adani anu atchula dzina lanu mwachabe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amayankhula za Inu ndi zolinga zoyipa; adani anu amagwiritsa ntchito dzina lanu molakwika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza anena za Inu moipa, Ndi adani anu achula dzina lanu mwacabe.