Psalms 139:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi sindidana nawo anthu odana nanu, Inu Chauta? Kodi sindinyansidwa nawo anthu okuukirani?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi sindidana nao iwo akudana ndi Inu, Yehova? Ndipo kodi sindimva nao chisoni iwo akuukira Inu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ine sindidana nawo amene amakudani, Inu Yehova? Kodi sindinyansidwa nawo amene amakuwukirani?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi sindidana nao iwo akudana ndi Inu, Yehova? Ndipo kodi sindimva nao cisoni iwo akuukira Inu?