Psalms 139:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimadana nawo ndi chidani chenicheni. Ndimaŵayesa adani anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidana nao ndi udani weniweni, ndiwayesa adani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndimadana nawo kwathunthu; ndi adani anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidana nao ndi udani weni weni: Ndiwayesa adani.