Psalms 139:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Fufuzeni, Inu Mulungu, kuti mudziŵe mtima wanga. Yeseni kuti mudziŵe maganizo anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundisanthule, Mulungu, nimudziwe mtima wanga; mundiyese nimudziwe zolingalira zanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Santhuleni, Inu Mulungu ndipo mudziwe mtima wanga; Yeseni ndipo mudziwe zolingalira zanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundisanthule, Mulungu, nimudziwe mtima wanga; Mundiyese nimudziwe zolingalira zanga.