Psalms 139:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mumandizinga kumbuyo ndi kutsogolo, ndipo mumandisanjika dzanja lanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munandizinga kumbuyo ndi kumaso, nimunaika dzanja lanu pa ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mumandizinga kumbuyo ndi kutsogolo komwe; mwasanjika dzanja lanu pa ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munandizinga kumbuyo ndi kumaso, Nimunaika dzanja lanu pa ine.