Psalms 139:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nzeru zimenezi nzopitirira nzeru zanga, nzapamwamba, sindingathe kuzimvetsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kudziwa ichi kundilaka ndi kundidabwitsa: Kundikhalira patali, sindifikirako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nzeru zimenezi ndi zopitirira nzeru zanga, ndi zapamwamba kuti ine ndizipeze.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kudziwa ici kundilaka ndi kundidabwiza: Kundikhalira patali, sindifikirako.