Psalms 139:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikaulukira kotulukira dzuŵa, kapena kukafika kuzambwe, ku mathero a nyanja,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikadzitengera mapiko a mbandakucha, ndi kukhala ku malekezero a nyanja;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati ndiwulukira kotulukira dzuwa, ngati ndikakhala ku malekezero a nyanja,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikadzitengera mapiko a mbanda kuca, Ndi kukhala ku malekezero a nyanja;