Psalms 14:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ai, anthu onse ndi osokera, onsewo ndi oipa chimodzimodzi. Palibe ndi mmodzi yemwe wochita zabwino, ai, palibiretu ndi mmodzi yemwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anapatuka onse; pamodzi anavunda mtima; palibe wakuchita bwino ndi mmodzi yense.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onse atembenukira kumbali, onse pamodzi asanduka oyipa; palibe amene amachita zabwino, palibiretu ndi mmodzi yemwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anapatuka onse; pamodzi anabvunda mtima; Palibe wakucita bwino ndi mmodzi yense.