Psalms 14:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kani anthu oipaŵa alibe nzeru chotere? Iwo amameza anthu anga, kuŵayesa chakudya, ndipo samutama Chauta mopemba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi onse ochita zopanda pake sadziwa kanthu? Pakudya anthu anga monga akudya mkate, ndipo saitana pa Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi anthu ochita zoyipawa sadziwa chilichonse? Akudya anthu anga ngati chakudya chawo ndipo satamanda Yehova?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi onse ocita zopanda pace sadziwa kanthu? Pakudya anthu anga monga akudya mkate, Ndipo saitana pa Yehova.