Psalms 14:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsonotu iwo adzachita mantha aakulu, pakuti Mulungu amakhala pa mbali ya anthu abwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepa anaopaopatu, pakuti Mulungu ali mu mbadwo wa wolungama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Awo ali apowo, agwidwa ndi mantha aakulu, pakuti Mulungu ali mʼgulu la olungama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepa anaopa-opatu: Pakuti Mulungu ali mu mbadwo wa wolungama.