Psalms 140:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pulumutseni, Inu Chauta, kwa anthu oipa. Tchinjirizeni kwa anthu ankhanza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo; Salimo la Davide. Ndilanditseni, Yehova, kwa munthu woipa; ndisungeni kwa munthu wachiwawa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Salimo la Davide. Landitseni Yehova kwa anthu oyipa; tetezeni kwa anthu ankhanza,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndilanditseni, Yehova, kwa munthu woipa; Ndisungeni kwa munthu waciwawa;