Psalms 140:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musalole kuti woononga mbiri ya mnzake akhazikike m'dziko. Choipa chimlondole munthu wankhanza mpaka kumuwononga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu wamlomo sadzakhazikika pa dziko lapansi; choipa chidzamsaka munthu wachiwawa kuti chimgwetse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musalole kuti anthu achipongwe akhazikike mʼdziko; choyipa chilondole anthu ankhanza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu wamlomo sadzakhazikika pa dziko lapansi; Coipa cidzamsaka munthu waciwawa kuti cimgwetse.