Psalms 140:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimadziŵa kuti Inu Chauta mumateteza ozunzika, mumaweruza mwachilungamo anthu osoŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidziwa kuti Yehova adzanenera wozunzika mlandu, ndi kuweruzira aumphawi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikudziwa kuti Yehova amapereka chiweruzo cholungama kwa anthu osauka, ndipo amateteza zolinga za anthu osowa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidziwa kuti Yehova adzanenera wozunzika mlandu, Ndi kuweruzira aumphawi,