Psalms 140:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo amalingalira mumtima mwao kuti achite zoipa, amautsa nkhondo nthaŵi zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene adzipanga zoipa mumtima mwao; masiku onse amemeza nkhondo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amene mu mtima mwawo amakonza zinthu zoyipa ndi kuyambitsa nkhondo tsiku lililonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amene adzipanga zoipa mumtima mwao; Masiku onse amemeza nkhondo.